Takulandirani ku WITH

Kulimbikitsa Maphunziro a Zamalonda a Azimayi ndi Atsikana mu Zokopa alendo ku Sub-Saharan Africa

PULOJEKITI IYI NDI YA NDANI?

Opindula ndi Pulojekiti ya WITH:

Atsikana (zaka 18-35); Aphunzitsi a sukulu za VET, Aphunzitsi a sukulu zina, kuphatikiza omwe ali pantchito zokopa alendo komanso kuchereza alendo.

Opindula ena mu maiko a ku SSA:

Sukulu za VET zaboma ndi za pulayiveti, ndi ena omwe amapereka maphunziro a VET. Mabungwe a zamalonda, za maluso, othandizira anthu a bizinesi ndi zina zotero.

Okhudzidwa ena:

Ochita malonda, eni mabizinesi ndi alangizi a zamalonda (makamaka azimayi), komanso makampani ndi mabizinesi omwe amagwira ntchito zokopa alendo. Opanga mfundo ndi ziganizo pankhani ya VET ndi ntchito zokopa alendo m'maiko a ku SSA kuphatikiza ma unduna ndi mabungwe aboma, komanso okonza mfundo, ma pulani ndi ziganizo pamlingo wapadziko lonse lapansi (EU ndi Africa).

ZOLINGA

1. Kulimbikitsa atsikana

pa luso lachikhalidwe kuti apambane ngati ochita malonda ndi eni bizinesi mu ntchito zokopa alendo..

2. Kuthandiza aphunzitsi a VET

pokonzanso chidziwitso chawo ndi machitidwe awo mogwirizana ndi zofunika pa msika wa ntchito ndi machitidwe apadziko lonse pa ntchito za chitukuko ndi ntchito zokopa alendo komanso kupeza njira zatsopano zoperekera maphunziro a VET.

3. Kulimbikitsa ndi kudziwitsa anthu

pa nkhani za ntchito zokopa alendo zokhazikika monga gawo la mapulogalamu a VET ndi maphunziro ena motero kupangitsa akatswiri azamalonda, ndi eni mabizinesi kukhala othandizira pachitukuko chokhazikika m'maiko a SSA.

4. Kulimbikitsa

njira zoperekera maphunziro ndi maluso a VET ndi kulimbikitsa mwayi wophunzira pochita mwayi kudzera mu kulumikizana kokhazikika pakati pa mabungwe aboma ndi mabungwe omwe amachita za VET ndi ena okhudzidwa komanso ogwira ntchito pamsika wantchito.

WITH

Kulimbikitsa Maphunziro a Zamalonda a Azimayi ndi Atsikana mu Zokopa alendo ku Sub-Saharan Africa

Zotsatira Zoyembekezeredwa

Zida Zophunzitsira za Pulojekiti ya WITH

Ndondomeko zophunzitsira za WITH

Tsamba la Maphunziro la WITH

Pulogalamu Yophunzitsa Aphunzitsi ya WITH

Buku la Aphunzitsi la WITH

Lipoti la Maphunziro a Aphunzitsi mu Pulojekiti ya WITH

Lipoti la Maphunziro a Atsikana ndi Azimayi

NEWSLETTERS

Knowledge Virtual Center

Electronic Newsletter 2

The WITH project has reached an important milestone with the implementation of the Capacity-Building Programme for VET trainers in May 2024. The Capacity-Building aimed to equip trainers with new pedagogical...

POSTER WITH

Electronic Newsletter 1

WITH is a two-year initiative that aims to skill and empower a new generation of climate and sustainability conscious women intrapreneurs, entrepreneurs and business owners to succeed in the tourism...

NKHANI

ny
Pitani ku Top